Mawu a M'munsi
b Ena amati kudzichekacheka kunali ngati kudzipereka nsembe. Zonse ziƔirizo zinkatanthauza kuti kudzivulaza kapena kukhetsa mwazi kungapangitse munthuyo kuyanjidwa ndi mulungu wake.