Mawu a M'munsi
d Mu 1938 anthu onse amene anafika pa Chikumbutso padziko lonse anali 73,420, ndipo anthu 39,225—53 peresenti ya onse amene analipo—anadya zizindikiro. Pofika 1998 chiŵerengero cha ofikapo chinakula kufika pa 13,896,312, pamene anthu 8,756 chabe ndiwo amene anadya, avareji ya wosakwanira pa munthu mmodzi ku mipingo 10 iliyonse.