Mawu a M'munsi a M’Baibulo lachigiriki lotchedwa Septuagint, verebu imodzimodzi imeneyo yomasuliridwa kuti “kukonza” inagwiritsidwa ntchito pa Salmo 17[16]:5, pamene Davide wokhulupirikayo anapemphera kuti mapazi ake ayendebe m’mabande a Yehova.