Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Katswiri wina ananena kuti phiphiritso lachihebrilo logwiritsidwa ntchito pa Mika 7:18 “linatengedwa pa zimene woyenda ulendo amachita pamene angodutsa molambalala chinthu chinachake chimene sakufuna kuchiyang’anitsitsa. Lingaliro limene phiphiritsolo likupereka si lakuti Mulungu saona tchimo, kapena kuti saliona ngati nkhani yaikulu, koma kuti saliyang’ana n’cholinga chopereka chilango; kuti sapereka chilango patchimolo, koma amalikhululukira.”​—Oweruza 3:26; 1 Samueli 16:8.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena