Mawu a M'munsi
a M’kaŵerengedwe ka madeti ka B.C.-A.D., zinthu zomwe zinachitika Yesu asanabadwe zimalembedwa kuti zinachitika m’zaka za m’ma “B.C.” (Kristu asanadze); zomwe zinachitika pambuyo pake zimalembedwa kuti zinachitika m’zaka za m’ma “A.D.” (Anno Domini—“m’chaka cha Ambuye wathu.”) Komabe, ophunzira ena amadigiri amakonda kugwiritsa ntchito kalembedwe ka anthu wamba ka “B.C.E.” (Nyengo Yathu isanafike) ndi “C.E.” (za M’nyengo Yathu.)