Mawu a M'munsi
a Arius (250-336 C.E.) anali wansembe wa chihelene amene anali kunena kuti Yesu anali wamng’ono pomuyerekeza ndi Atate. Bungwe logamula lotchedwa Nicaea linakana malingaliro ake m’chaka cha 325 C.E.—Onani Galamukani! yachingelezi ya June 22, 1989, tsamba 27.