Mawu a M'munsi
a Zinthu zimene zinaperekedwa pomanga kachisi wa Solomo zingalingane ndi ndalama zokwanira madola 40,000,000,000 pamitengo yamasiku ano. Zonse zimene sizinagwiritsidwe ntchito pantchito yomangayo zinaikidwa mosungiramo chuma m’kachisimo.—1 Mafumu 7:51.