Mawu a M'munsi
a Buku lakuti The Finished Mystery linali lachisanu ndi chiƔiri pa mavoliyumu angapo omwe onse pamodzi amatchedwa Studies in the Scriptures, asanu ndi limodzi oyambirira analembedwa ndi Charles Taze Russell. The Finished Mystery linasindikizidwa pambuyo pa imfa ya Russell.