Mawu a M'munsi
b Chihebri ndi chiyankhulo chopanda zilembo za mawu. Zilembo za mawu zimaikidwamo ndi woŵerenga malinga ndi nkhani yake. Ngati nkhani yake yanyalanyazidwa, tanthauzo la liwu lingasinthiretu mwa kuikamo zilembo zina za mawu. Mawu a m’Chingelezi ali ndi zilembo zakezake za mawu, zomwe zimapangitsa kufufuza mawu koteroko kukhala kovuta kwambiri.