Mawu a M'munsi
a Malinga ndi Chilamulo cha Mose, wakuba ankayenera kubwezera kuŵirikiza kawiri, kanayi, kapena kuŵirikiza kasanu. (Eksodo 22:1-4) Mawu akuti “kasanu ndi kaŵiri” mwachionekere akutanthauza chilango cha kalavula gaga, chomwe chingathe kukhala kuŵirikiza kambirimbiri zomwe anali atabazo.