Mawu a M'munsi
a Ngati mukufuna nkhani yolongosola chifukwa chimene Mulungu walolera zoipa kumwamba ndi padziko lapansi, onani buku lakuti Chidziŵitso Chotsogolera ku Moyo Wosatha, lofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc., m’masamba 70-9.