Mawu a M'munsi
b Mosiyana ndi ubwenzi wapakati pa anthu, ubwenzi ndi Mulungu n’ngwozikika pa chikhulupiriro cha kukhalapo kwake. (Ahebri 11:6) Kuti mumve zambiri zokhudza kulimbitsa chikhulupiriro mwa Mulungu, chonde onani buku lakuti, Is There a Creator Who Cares About You?, lofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.