Mawu a M'munsi
b Makomiti Olankhulana ndi Chipatala (HLC), amaimira Mboni za Yehova padziko lonse, ndi kuthandiza kukhazikitsa mgwirizano pakati pa odwala ndi achipatala. Amaperekanso njira zina zochiritsira zopezeka pa kufufuza kwatsopano kwa zamankhwala.