Mawu a M'munsi
a Dipatimenti Yopereka chidziŵitso cha Zachipatala imayang’anira ntchito ya padziko lonse ya Makomiti Olankhulana ndi Chipatala. Makomiti ameneŵa nawonso amakhala ndi Akristu odzipereka omwe anaphunzitsidwa kulimbikitsa mgwirizano pakati pa madokotala ndi Mboni zodwala. Pali Makomiti Olankhulana ndi Chipatala okwana 1,400 omwe akuthandiza odwala m’mayiko oposa 200.