Mawu a M'munsi
a Pamndandanda wa zinthu zoposa 40 zosautsa mtima kwambiri pamoyo wa munthu zimene Dr. Thomas Holmes ndi Dr. Richard Rahe anasanja, pamalo atatu oyambirira anaikapo imfa ya mnzako wa m’banja, kusudzulana, ndi kupatukana. Kukwatira kuli panambala seveni.