Mawu a M'munsi
a Buku la Insight on the Scriptures (lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova) limanena kuti, “mipukutu yamakedzana imasimba za Farao amene analamula amuna okhala ndi zida kukagwira mkazi wokongola ndi kupha mwamuna wake.” Choncho sikuti Abramu ankachita mantha pachabe.