Mawu a M'munsi
a Nkhani zosimba zimene ena anakumana nazo zimene zili m’nkhani ino ndi nkhani yotsatira zingakhale za kumayiko amene chikhalidwe chawo n’chosiyana ndi chanu. Yesani kupeza mfundo zake za nkhanizo ndi kuzigwiritsa ntchito pa chikhalidwe chanu.