Mawu a M'munsi
a M’Chihebri, “liwu lakuti “mphuno” (ʼaph) nthaŵi zambiri amaligwiritsa ntchito mophiphiritsa kutanthauza mkwiyo. Amatero chifukwa cha kupuma kwa wefuwefu kwa munthu woti wapsa mtima kwambiri.