Mawu a M'munsi
a Amene analemba Malemba Achigiriki Achikristu sanafotokoze kuti Salmo limeneli likunena za ulosi wa Mesiya. N’zoona kuti Yehova anali pothaŵirapo ndi linga kwa Yesu Kristu, monga mmene alili kwa otsatira a Yesu odzozedwa ndi anzawo amene adzipatulira kwa Mulungu monga gulu mu “nthaŵi ya chimaliziro” ino.—Danieli 12:4.