Mawu a M'munsi
a Malinga ndi buku lakuti The Catholic Encyclopedia, m’nyengo ya kukonzanso zinthu ya Reformation, kuumiriza anthu kutsatira chipembedzo chinachake ankakufotoza m’mawu a Chilatini amene kwenikweni amatanthauza kuti: “Amene akulamulira dziko ndi amenenso amasankha chipembedzo cha dzikolo.”