Mawu a M'munsi
b Cha m’ma 1199, bishopu wa ku Metz, kumpoto chakum’maŵa kwa dziko la France, anadandaula kwa Papa Innocent Wachitatu kuti anthu anali kuŵerenga ndiponso kukambirana Baibulo m’chinenero chawo. Mwachionekere, bishopu ameneyo ankanena za Awadensi.