Mawu a M'munsi
d Chifukwa chodzudzulidwa kosalekeza, Awadensi anayamba kutchedwa ndi dzina loti vauderie (dzina lochokera ku mawu achifalansa akuti vaudois). Dzinali limaperekedwa kwa anthu omwe akuwaganizira kuti ndi ampatuko olambira Mdyerekezi.