Mawu a M'munsi
a Akristu ayenera kuyesetsa kulimbikitsa mtendere, mogwirizana ndi malangizo amene ali pa Mateyu 5:23, 24. Ngati nkhaniyo ndi yokhudza machimo aakulu, Mkristu ayenera kuyesetsa kubweza mbale wake, monga mmene akufotokozera pa Mateyu 18:15-17. Onani Nsanja ya Olonda ya October 15, 1999 masamba 17-22.