Mawu a M'munsi
c Mawu omalizaŵa amene ali pa Machitidwe 20:35, anawagwira mawu ndi mtumwi Paulo yekha, ngakhale kuti mfundo ya mawuwo imapezeka m’Mauthenga Abwino. Mwina Paulo anamva mawu ameneŵa kwa munthu wina (mwina wophunzira amene anamva Yesu akunena zimenezi kapena anamva kwa Yesu woukitsidwa) kapena Mulungu anam’vumbulutsira.—Machitidwe 22:6-15; 1 Akorinto 15:6, 8.