Mawu a M'munsi
d Ayuda chaka chilichonse ankafunika kupereka ndalama ya msonkho wa pakachisi yokwana rupiya (ndalama yokwanira kulipira munthu masiku aŵiri). Ndalama ya msonkhoyi ankaigwiritsa ntchito kukonzetsera kachisi, kulipirira ntchito imene inali kuchitika pakachisipo ndiponso nsembe zimene anali kupereka kumeneko m’malo mwa mtundu wonsewo.