Mawu a M'munsi
b Yeremiya 38:19 amavumbula kuti Ayuda ambiri ‘ananka’ kwa Akasidi ndipo sanaphedwe koma anawatengera ku ukapolo. Sitikudziwa ngati anadzipereka potsatira mawu a Yeremiya. Komabe, kupulumuka kwawo kunatsimikizira mawu a mneneriyo.