Mawu a M'munsi
a Buku lakuti World Book Encyclopedia limati kutchova njuga ndiko “kubetcherana pa zotsatira za maseŵero, zochitika, kapena zinthu zomwe zingachitike mwamwayi.” Limafotokozanso kuti “otchova njuga nthaŵi zambiri amabetcherana ndalama pa . . . maseŵero oyendera mwayi monga malotale, maseŵero a makadi, ndi mayere.”