Mawu a M'munsi
a Nthaŵi zambiri, munthu wachidwi amene akuphunzira bulosha la Mulungu Amafunanji, akamaliza amayamba kuphunzira buku la Chidziŵitso Chotsogolera ku Moyo Wosatha. Mabuku onseŵa ndi ofalitsidwa ndi Mboni za Yehova. Malingaliro amene aperekedwa apa adzathandiza kuthetsa zopinga zimene zingabwezere m’mbuyo kupita patsogolo kwauzimu.