Mawu a M'munsi
c Mabaibulo angapo a Chispanya ndi a Chikataloniya ndi osiyana kwambiri ndi mabaibulo ena chifukwa amamasulira zilembo zinayi zoimira dzina la Yehova m’Chihebri, pogwiritsira ntchito mawu akuti “Yavé,” “Yahveh,” “Jahvè,” ndi “Jehová.”