Mawu a M'munsi
b Pofotokoza za liwu la Chigiriki limene analimasulira kuti “dikirani,” wolemba mabuku otanthauzira mawu, W. E. Vine anafotokoza kuti liwulo kwenikweni limatanthauza ‘kuthamangitsa tulo,’ ndipo “silimangosonyeza kukhala maso chabe, koma kukhala tcheru, makamaka anthu amene ali ndi cholinga pa chinthu chinachake.”