Mawu a M'munsi
a Ngakhale kuti nthambi za mpesa mu fanizo zimaimira atumwi a Yesu ndi Akristu ena amene adzakhala ndi malo mu Ufumu wa Mulungu wakumwamba, fanizoli lili ndi choonadi chimene onse amene ali otsatira a Kristu masiku ano angapindule nacho.—Yohane 3:16; 10:16.