Mawu a M'munsi
a M’chaka chaposachedwapa, mipingo ya Mboni za Yehova sinali kulalikira mokhazikika malo oposa 8 peresenti a gawo lonse la ku Mexico. Zimenezi zikutanthauza kuti pali anthu oposa 8,200,000 amene akukhala mu madera mmene kulalikira kuli kochepa.