Mawu a M'munsi a “Anthu Akunyanja” ameneŵa nthaŵi zambiri anali anthu oyenda panyanja ochokera ku zilumba za ku Mediterranean ndi m’madera a m’mphepete mwa nyanjayi. Mwina Afilisti anali ena mwa iwo.—Amosi 9:7.