Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

b Ngakhale kuti pali maganizo osiyana, ena amati kachisi wa Dagani ndiye kachisi wa El. Roland de Vaux, katswiri wa maphunziro komanso pulofesa wachifalansa pa Sukulu ya ku Yerusalemu Yophunzitsa Baibulo, anati Dagani, amene pa Oweruza 16:23 ndi pa 1 Samueli 5:1-5 amutchula kuti Dagoni, ndiye dzina lake lenileni la El. Buku lina lakuti The Encyclopedia of Religion limati n’zotheka kuti “Dagani mwa njira ina anali kugwirizanitsidwa kapena anaphatikizana ndi [El].” M’zolemba za ku Ras Shamra, Baala amatchedwa mwana wa Dagani, koma sizikudziŵika kuti anatanthauza chiyani ponena kuti “mwana.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena