Mawu a M'munsi
a Kuti mumve zambiri zokhudza mbiri ya Mboni za Yehova m’Malawi, onani bulosha lakuti Mboni za Yehova m’Malaŵi—Nkhani ya Kukhulupirika Kwawo; kapena buku la 1999 Yearbook of Jehovah’s Witnesses, masamba 149-223, zofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.