Mawu a M'munsi
a Zinthu zikafika poipa, pangakhale chifukwa chomveka chakuti anthu okwatirana apatukane. (1 Akorinto 7:10, 11; onani buku la Chinsinsi cha Chimwemwe cha Banja, masamba 160-161, losindikizidwa ndi Mboni za Yehova.) Komanso, Baibulo limalola kusudzulana pachifukwa cha chigololo (chisembwere).—Mateyu 19:9.