Mawu a M'munsi
a Kuchokera ku mawu a Chilatini akuti utraque, otanthauza kuti “chilichonse mwa ziŵiri.” Mosiyana ndi ansembe a tchalitchi cha Roma Katolika omwe sankapereka vinyo kwa akristu awo pamwambo wa Misa, a Utraquists (magulu osiyanasiyana a Ahusi) ankapereka mkate ndi vinyo.