Mawu a M'munsi
c Baibulo limasonyeza kuti Yerusalemu anagwa zaka 70 Ayuda amene anagwidwa ukapolo asanabwerere kwawo mu 537 B.C.E. (Yeremiya 25:11, 12; Danieli 9:1-3) Kuti muone nkhani yatsatanetsatane ya “nthaŵi zawo za anthu akunja,” onani masamba 231 mpaka 233 a buku la Kukambitsirana za m’Malemba, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.