Mawu a M'munsi
a Pamfundo ya kapangidwe ka mneni amene anam’tembenuza kuti “wonyenga” pa Chivumbulutso 12:9, buku lina linanena kuti “amasonyeza ntchito yopitirira yomwe yakhala chizoloŵezi.”