Mawu a M'munsi
c Nebrija amatchedwa munthu woyamba kumenyera ufulu wa anthu ku Spain (katswiri wa maphunziro womva za ena). M’chaka cha 1492 anafalitsa buku loyamba lakuti Gramática castellana (Galamala ya Chinenero cha Chikasitilia). Patapita zaka zitatu, anaganiza zogwiritsa ntchito moyo wake wonse kuphunzira Malemba Opatulika.