Mawu a M'munsi
a Buku lina lotanthauzira mawu lakuti The New Oxford Dictionary of English, limatanthauzira mawu akuti ndale kuti ndi “zochitika zokhudza kayendetsedwe ka dziko kapena dera, makamaka kutsutsana kapena kulimbana pakati pa anthu kapena zipani zomwe zili ndi mphamvu kapena zomwe zikufuna kupeza mphamvu.”