Mawu a M'munsi
a Buku lina limanena kuti lamulo la kubatiza ndi kuphunzitsa “sikuti kwenikweni limanena za . . . ntchito ziŵiri zimene zimachitika motsatizana.” Koma, “kuphunzitsa ndi ntchito imene imayamba munthu asanabatizidwe . . . ndipo imapitirirabe munthu akabatizidwa.”