Mawu a M'munsi
a Mu ulosi wa Yesaya, Yehova mwiniyo akufotokozedwa kuti wavala “chilungamo monga chida cha pachifuwa.” Motero, iye amafuna kuti oyang’anira m’mipingo azichita zinthu mwachilungamo.—Yesaya 59:14, 15, 17.