Mawu a M'munsi
a Kuti mumve tsatanetsatane wa mmene zinthu zakumwamba zimene timaziona zimasonyezera kuti Mulungu ndi wanzeru ndiponso ndi wamphamvu, ŵerengani machaputala 5 ndi 17 m’buku lakuti Yandikirani kwa Yehova, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.