Mawu a M'munsi
a Malangizo othandiza a m’Baibulo pankhani zimenezi ndiponso nkhani zina zofunikira mungawapeze m’buku lakuti Mafunso Achichepere Akufunsa—Mayankho Amene Amathandiza ndi lakuti Chinsinsi cha Chimwemwe cha Banja, omwe amafalitsidwa ndi Mboni za Yehova.