Mawu a M'munsi
a Ngati mukufuna kudziwa bwino za malemba amene ena amati amatsutsana, ndiponso kuti muone kugwirizana kwawo, mungapeze zitsanzo zambiri za malemba oterewa m’mutu 7 wa buku lakuti Baibulo—Kodi Ndilo Mawu a Mulungu Kapena a Munthu? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.