Mawu a M'munsi
a Mwa kungosintha chilembo chimodzi chokha, malemba achihebri angamveke ngati akunena kuti “anawalowetsa m’macheka” kapena kuti “anawadula zidutswazidutswa (ndi macheka).” Komanso mawu akuti “uvuni ya njerwa” angatanthauzenso “chikombole cha njerwa.” Chikombole chotere chinali chaching’ono kwambiri mwakuti munthu sangakwanemo.