Mawu a M'munsi
a Galileo anaputa dala udani waukulu chifukwa ankayankha mwam’topola ndiponso mwachipongwe. Komanso ponena kuti mfundo ija n’njogwirizana ndi Malemba, anakhala ngati akunena kuti iyeyo ndiye akudziwa bwino nkhani yachipembedzo, ndipotu izi zinangowonjezera mkwiyo wa tchalitchicho.