Mawu a M'munsi
a M’zaka za m’ma 200 B.C.E., Mgiriki wina dzina lake Aristarchus wa ku Samos anayambitsa mfundo yakuti dzuwa ndilo lili pakati pa chilengedwe chonse, koma anthu anatsutsa zimenezi n’kutsatira mfundo ya Aristotle.