Mawu a M'munsi a Pamene nkhaniyi inali kukonzedwa, Erna Ludolph anamwalira ali ndi zaka 96, ali wokhulupirikabe.